Luke 10:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye adati, “Iwe Marita iwe, ukutekeseka nkuvutika ndi zinthu zambiri,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Ambuye anayankha nati kwa iye, Marita, Marita, uda nkhawa nuvutika ndi zinthu zambiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye anati, “Marita, Marita, ukudandaula ndi kuvutika ndi zinthu zambiri,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Ambuye anayankha nati kwa iye, Marita, Marita, uda nkhawa nubvutika ndi zinthu zambiri;