Luke 11:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pakabwera wina wamphamvu zoposa, namgonjetsa, amalanda zida zimene ankazidalirazo, nkugaŵagaŵa katundu amene walandayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma pamene paliponse amdzera wakumposa mphamvu, nakamlaka, amchotsera zida zake zonse zimene anazitama, nagawa zofunkha zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pakabwera wina wamphamvu zoposa namugonjetsa, amalanda zida zimene munthuyo amazidalirazo ndi kugawa katundu wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma pamene pali ponse amdzera wakumposa mphamvu, nakamlaka, amcotsera zida zace zonse zimene anazitama, nagawa zofunkha zace.