Luke 11:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yesu adati, “Iyai, odala ndi anthu amene amamva mau a Mulungu naŵagwiritsa ntchito.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Iye anati, Inde, koma odala iwo akumva mau a Mulungu, nawasunga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yesu anayankha kuti, “ Odala ndi amene amamva mawu a Mulungu ndi kuwasunga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye anati, Inde, koma odala iwo akumva mau a Mulungu, nawasunga.