Luke 11:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yesu adatsiriza kulankhula, wina wa m'gulu la Afarisi adamuitana kuti akadye naye. Tsono Yesu adaloŵa m'nyumba nakakhala podyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pakulankhula Iye, anamuitana Mfarisi kuti adye naye; ndipo analowa naseama kudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu atamaliza kuyankhula, Mfarisi wina anamuyitana kuti akadye naye. Tsono Yesu analowa mʼnyumba ndi kukhala podyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pakulankhula iye, anamuitana Mfarisi kuti adye naye; ndipo analowa naseama kudya.