Luke 11:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfarisiyo adadabwa poona kuti Yesu wayamba kudya osatsata mwambo wao wa kasambidwe ka m'manja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anazizwa Mfarisiyo, pakuona kuti anayamba chakudya asanasambe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfarisiyo anadabwa atazindikira kuti Yesu anayamba kudya wosatsata mwambo wawo wakasambidwe ka mʼmanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anazizwa Mfarisiyo, pakuona kuti anayamba cakudya asanasambe.