Luke 11:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinu anthu opusa! Kodi Mulungu amene adapanga zakunja, si yemweyo adapanganso zam'kati?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Opusa inu, kodi Iye wopanga kunja kwake sanapangenso m'kati mwake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu opusa inu! Kodi amene anapanga zamʼkati sanapangenso zakunja?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Opusa inu, kodi iye wopanga kunja kwace sanapanganso m'kati mwace?