Luke 11:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muli ndi tsoka, chifukwa mumamanga ziliza za aneneri, pamene ndi makolo anu omwe akale amene adapha aneneriwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsoka inu! Chifukwa mumanga za pa manda a aneneri, ndipo makolo anu anawapha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsoka kwa inu, chifukwa mumawaka manda a aneneri, komatu ndi makolo anu amene anawapha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsoka inu! cifukwamumanga za pa manda a aneneri, ndipo makolo anu anawapha.