Luke 11:54 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Cholinga chao chinali chofuna kumtapa m'kamwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
namlindira akakole kanthu kotuluka m'kamwa mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pofuna kumukola muchina chilichonse chimene Iye angayankhule.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
4 namlindira akakole kanthu koturuka m'kamwa mwace.