Luke 12:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja zimenezi amazifunafuna ndi anthu a mitundu yonse yapansipano. Atate anu amadziŵa kuti mumazisoŵa zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti izi zonse mitundu ya anthu a pa dziko lapansi amazifunafuna; koma Atate wanu adziwa kuti musowa zimenezi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti anthu akunja amathamanga kufunafuna zinthu zotere, ndipo Atate amadziwa kuti mumazifuna zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti izi zonse mitundu ya anthu a pa dziko lapansi amazifunafuna; koma Atate wanu adziwa kuti musowa zimenezi.