Luke 12:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma kumbukirani kuti, mwini nyumba akadadziŵiratu nthaŵi yoti mbala ifika, sibwenzi atalola kuti ithyole nyumba yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma zindikirani ichi, kuti mwini nyumba akadadziwa nthawi yake yakudza mbala, akadadikira, ndipo sakadalola nyumba yake ibooledwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma zindikirani izi: Ngati mwini nyumba akanadziwa ora limene mbala ibwera, sakanalola kuti nyumba yake ithyoledwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma zindikirani ici, kuti mwini nyumba akadadziwa nthawi yace yakudza mbala, akadadikira, ndipo sakadalola nyumba yace ibooledwe.