Luke 12:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho inunso khalani okonzeka, pakuti Mwana wa Munthu adzabwera pa nthaŵi imene simukuyembekeza.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Khalani okonzeka inunso; chifukwa nthawi imene simulingirira, Mwana wa Munthu akudza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inunso muyenera kukhala okonzeka, chifukwa Mwana wa Munthu adzabwera pa ora limene simukumuyembekezera Iye.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Khalani okonzeka inunso; cifukwa nthawi imene simulingirira, Mwana wa munthu akudza.