Luke 12:44 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu ndikunenetsa kuti adzamuika woyang'anira chuma chake chonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinena ndinu zoona, kuti adzamuika iye kapitao wa pa zonse ali nazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zoonadi, Ine ndikukuwuzani kuti adzamuyika kukhala woyangʼanira katundu wake yense.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
1 Ndinena ndinu zoona, kuti adzamuika iye kapitao wa pa zonse ali nazo.