Luke 12:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Wantchito amene akudziŵa zimene mbuye wake amafuna, koma osakonzekera kuzichita, adzamkwapula kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kapolo uyo, wodziwa chifuniro cha mbuye wake, ndipo sanakonza, ndi kusachita zonga za chifuniro chakecho, adzakwapulidwa mikwapulo yambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Wantchito amene amadziwa chifuniro cha mbuye wake koma wosakonzeka kapena wosachita chimene mbuye wake akufuna adzakwapulidwa zikwapu zambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo 4 kapolo uyo, wodziwa cifuniro ca mbuye wace, ndipo sanakonza, ndi kusacita zonga za cifuniro caceco, adzakwapulidwa mikwapulo yambiri.