Luke 12:50 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ndiyenera kuyamba ndaloŵa m'masautso akulu, ndipo mtima wanga sukhazikika mpaka zitachitika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndili ndi ubatizo ndikabatizidwe nao; ndipo ndikanikizidwa Ine kufikira ukatsirizidwa!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Ine ndiyenera kubatizidwa, ndipo ndikusautsika mu mtima mpaka utachitika!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndiri ndi ubatizo ndikabatizidwe nao; ndipo ndikanikizidwa Ine kufikira ukatsirizidwa!