Luke 12:54 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adauzanso anthu onse aja kuti, “Mukaona mtambo ukukwera kuzambwe, pompo mumati, ‘Mvula ikubwera,’ ndipo imabweradi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Iye ananenanso kwa makamu a anthu, Pamene paliponse muona mtambo wokwera kumadzulo, pomwepo munena, kuti, Ikudza mvula; ndipo itero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anati kwa gulu la anthu, “Pamene mukuona mtambo ukukwera kummawa, nthawi yomweyo inu mumati, ‘kugwa mvula,’ ndipo imagwadi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye ananenanso kwa makamu a anthu, 7 Pamene pali ponse muona mtambo wokwera kumadzulo, pomwepo munena, kuti, Ikudza mvula; ndipo itero.