Luke 12:59 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu ndikunenetsa kuti sudzatulukamo mpaka utalipira zonse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndinena kwa iwe, Sudzatulukamo konse kufikira utalipira kakobiri kukumaliza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikuwuzani kuti, simudzatulukamo mpaka mutalipira ndalama zonse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndinena kwa iwe, 9 Sudzaturukamo konse kufikira utalipira kakobiri kakumariza.