Luke 13:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adatinso, “Ndingayerekezenso ndi chiyani Ufumu wa Mulungu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiponso anati, Ndidzafanizira Ufumu wa Mulungu ndi chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anafunsanso kuti, “Kodi ufumu wa Mulungu ndingawufanizire ndi chiyani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiponso anati, Ndidzafanizira Ufumu wa Mulungu ndi ciani?