Luke 14:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yesu adamuphera fanizo, adati, “Munthu wina adaakonza phwando lalikulu, naitana anthu ambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anati kwa iye, Munthu wina anakonza phwando lalikulu; naitana anthu ambiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anayankha kuti, “Munthu wina ankakonza phwando lalikulu ndipo anayitana alendo ambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anati kwa iye, Munthu wina anakonza phwando lalikuru; naitana anthu ambiri;