Luke 14:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo wina adati, ‘Ndangokwatira tsopano apa, choncho sinditha kubwera.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati wina, Ine ndakwatira mkazi, ndipo chifukwa chake sindingathe kudza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Wina anatinso, ‘Ine ndangokwatira kumene, choncho sinditha kubwera.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati wina, Ine ndakwatira mkazi, ndipo cifukwa cace sindingathe kudza.