Luke 14:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aliyense amene sasenza mtanda wake nkumanditsata, sangakhale wophunzira wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amene aliyense sasenza mtanda wake wa mwini yekha, ndi kudza pambuyo panga, sakhoza kukhala wophunzira wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo aliyense amene sasenza mtanda wake ndi kunditsata Ine sangakhale ophunzira wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amene ali yense sasenza mtanda wace wa mwini yekha, ndi kudza pambuyo panga, sakhoza kukhala wophunzira wanga,