Luke 14:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzati, ‘Mkulu uyu adaayamba kumanga nyumba, koma adalephera kuitsiriza.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kunena kuti, Munthu uyu anayamba kumanga, koma sanathe kumaliza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nanena kuti, ‘Munthu uyu anayamba kumanga koma sanathe kutsiriza.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kunena kuti, Munthu uyu anayamba kumanga, koma sanathe kumariza.