Luke 14:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mchere ndi wabwino. Koma ngati mcherewo watha mphamvu, mphamvu zakezo nkuzibwezeranso nchiyani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kotero mchere uli wokoma; koma ngati mchere utasukuluka adzaukoleretsa ndi chiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mchere ndi wabwino, koma ngati usukuluka adzawukoleretsanso ndi chiyani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kotero mcere uli wokoma; koma ngati mcere utasukuluka adzaukoleretsa ndi ciani?