Luke 15:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse okhometsa msonkho ndi Ayuda enanso onyozera Malamulo ankabwera kwa Yesu kudzamva mau ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma amisonkho onse ndi anthu ochimwa analikumyandikira kudzamva Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano amisonkho ndi “ochimwa” ankasonkhana kudzamvera mawu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma amisonkho onse ndi anthu ocimwa analikumyandikira kudzamva iye.