Luke 15:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adatinso, “Munthu wina adaali ndi ana aamuna aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anati, Munthu wina anali ndi ana amuna awiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesu anapitiriza kunena kuti, “Panali munthu amene anali ndi ana aamuna awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anati, Munthu wina anali ndi ana amuna awiri;