Luke 15:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo katengeni mwanawang'ombe wonenepa uja, muphe kuti tidye, tikondwere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo idzani naye mwanawang'ombe wonenepa, mumuphe, ndipo tidye, tisekere;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bweretsani mwana wangʼombe wonenepa ndipo iphani. Tiyeni tikhale ndi phwando ndi kukondwerera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo idzani naye mwana wa ng'ombe wonenepa, mumuphe, ndipo tidye, tisekere;