Luke 15:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaitana wantchito mmodzi namufunsa kuti, ‘Kodi kwagwanji?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaitana mmodzi wa anyamata, namfunsa, Zinthu izi nzotani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo iye anayitana mmodzi wa antchito, namufunsa chimene chimachitika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaitana mmodzi wa anayamata, namfunsa, Zinthu izi nzotani?