Luke 15:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamva zimenezo mwana wamkuluyo adapsa mtima, nakana kuloŵa. Apo bambo wake adatuluka, nkumupempha mopemba kuti aloŵe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anakwiya, ndipo sanafune kulowamo. Ndipo atate wake anatuluka namdandaulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mwana wamkulu anakwiya ndipo anakana kulowa. Chomwecho abambo ake anatuluka ndi kumudandaulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anakwiya, ndipo sanafuna kulowamo, Ndipo atate wace anaturuka namdandaulira.