Luke 15:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Bambo wakeyo adamuyankha kuti, ‘Mwana wanga, iwe uli ndi ine nthaŵi zonse, ndipo zanga zonse nzako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iye ananena naye, Mwana wanga, iwe uli ndine nthawi zonse, ndipo zanga zonse zili zako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abambowo anati, “Mwana wanga, iwe umakhala ndi ine nthawi zonse ndipo zonse ndili nazo ndi zako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iye ananena nave, Mwana wanga, iwe uli ndine nthawi zonse, ndipo zanga zonse ziri zako.