Luke 16:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Apo wachuma uja adati, ‘Ndipotu ndikukupemphani atate, kuti mumtume Lazaroyo apite ku nyumba ya bambo wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anati, Pamenepo ndikupemphani, Atate, kuti mumtume kunyumba ya atate wanga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Iye anayankha kuti, ‘Ndipo ndikupemphani inu, abambo, mutumeni Lazaro ku nyumba ya abambo anga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anati, Pamenepo ndikupemphani, Atate, kuti mumtume ku nyumba ya atate wanga;