Luke 17:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Afarisi ena adafunsa Yesu kuti, “Kodi Mulungu adzakhazikitsa liti ufumu wake?” Yesu adaŵayankha kuti, “Mulungu sakhazikitsa ufumu wake mooneka ndi maso ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene Afarisi anamfunsa Iye, kuti, Ufumu wa Mulungu ukudza liti, anawayankha, nati, Ufumu wa Mulungu sukudza ndi maonekedwe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Afarisi atamufunsa Iye kuti, ufumu wa Mulungu udzabwera liti, Yesu anayankha kuti, “Mulungu sakhazikitsa ufumu wake mooneka ndi maso,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene Afarisi anamfunsa iye, kuti, Ufumu wa Mulungu ukudza liti, anawayarikha, nati, Ufumu wa Mulungu sukudza ndi maonekedwe;