Luke 17:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adauza ophunzira ake kuti, “Akudza masiku pamene mudzalakalaka kuwona nthaŵi ya kudza kwa Mwana wa Munthu ngakhale tsiku limodzi lokha, koma simudzaloledwa ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa ophunzira ake, Adzadza masiku, amene mudzakhumba kuona limodzi la masiku a Mwana wa Munthu, koma simudzaliona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Iye anati kwa ophunzira ake, “Masiku akubwera pamene inu mudzalakalaka mutaona tsiku limodzi la masiku a Mwana wa Munthu, koma simudzaliona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa ophunzira ace, Adzadza masiku, amene mudzakhumba kuona limodzi la masiku a Mwana wa munthu, koma simudzaliona.