Luke 17:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu azidzakuuzani kuti, ‘Suuwo uli uko,’ kapena, ‘Suuwu uli pano,’ musadzapiteko kapena kuŵatsatira ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzanena ndi inu, Taonani ilo! Taonani ili? Musachoka kapena kuwatsata;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu adzakuwuzani kuti, ‘Uyo ali apoyo!’ kapena ‘Uyu ali apa!’ Musawathamangire iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzanena ndi inu, Taonani ilo! taonani ili! musacoka kapena kuwatsata;