Luke 17:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu monga mphezi imang'anipa nkuŵala kuchokera mbali ina ya kuthambo kufikira mbali yake ina, Mwana wa Munthu adzateronso pa tsiku la kubwera kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti monga mphezi ing'anipa kuchokera kwina pansi pa thambo, niunikira kufikira kwina pansi pa thambo, kotero adzakhala Mwana wa Munthu m'tsiku lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti monga mphenzi ingʼanima ndi kuwala kuchokera mbali ina ya thambo kufikira inzake, koteronso adzakhala ali Mwana wa Munthu pa tsiku lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti monga mphezi ing'anipa kucokera kwina pansi pa thambo, niunikira kufikira kwina pansi pa thambo, kotero adzakhala Mwana wa munthu m'tsiku lace.