Luke 17:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Iye ayenera kuti ayambe wamva zoŵaŵa zambiri, ndipo kuti anthu amakono amkane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ayenera athange wamva zowawa zambiri nakanidwe ndi mbadwo uno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma poyamba ayenera kuzunzika mu zambiri ndi kukanidwa ndi mʼbado uno.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ayenera athange wamva zowawa zambiri nakanizidwe ndi mbadwo uno.