Luke 17:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ungamthokoze wantchitoyo chifukwa chakuti wachita zimene unamlamula?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi ayamika kapoloyo chifukwa anachita zolamulidwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi iye angathokoze wantchitoyo chifukwa chochita chimene anawuzidwa kuchita?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi ayamika kapoloyocifukwa anacita zolamulidwa?