Luke 18:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamene munthu uja adamva zimenezi, adavutika mu mtima, pakuti adaali wolemera kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pakumva izi anagwidwa nacho chisoni chambiri; pakuti anali mwini chuma chambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamva zimenezi, anakhumudwa kwambiri chifukwa anali munthu wachuma chambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pakumva izi anagwidwa naco cisoni cambiri; pakuti anali mwini cuma cambiri.