Luke 18:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene adamva zimenezi adafunsa kuti, “Tsono nanga angathe kupulumuka ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akumvawo anati, Tsono ndani angathe kupulumutsidwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene anamva izi anafunsa kuti, “Nanga ndani amene angapulumuke?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akumvawo anati, Tsono ndani angathe kupulumutsidwa?