Luke 18:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ameneyo pansi pompano adzalandira zonsezo mochuluka kwambiri koposa kale, kenaka kutsogoloko adzalandira moyo wosatha.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma adzalandira zobwezedwa koposatu m'nthawi yino; ndipo m'nthawi ilinkudza moyo wosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
adzalephera kulandira mowirikiza mʼmoyo uno, ndi mʼmoyo ukubwerawo, moyo wosatha.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma adzalandira zobwezedwa koposatu m'nthawi yino; ndipo m'nthawi irinkudza moyo wosatha.