Luke 19:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu Mwana wa Munthu adabwera kudzafunafuna ndi kudzapulumutsa amene adatayika.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Mwana wa Munthu anadza kufunafuna ndi kupulumutsa chotayikacho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pajatu Mwana wa Munthu anabwera kudzafunafuna ndi kupulumutsa chotayikacho.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Mwana wa munthu anadza kufunafuna ndi kupulumutsa, cotayikaco.