Luke 19:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Woyamba adadza nati, ‘Ambuye, ndalama yanu ija idapindula ndalama makumi khumi.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anafika woyamba, nanena, Mbuye, mina yanu inachita nionjeza mina khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Woyamba anabwera ndipo anati, ‘Bwana ndalama zanu zapindula khumi zina.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anafika woyamba, nanena, Mbuye ndalama yanu inacita nionjeza ndalama khumi.