Luke 19:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wachiŵiri adadza nati, ‘Ambuye, ndalama yanu ija idapindula ndalama makumi asanu.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadza wachiwiri, nanena, Mbuye, mina yanu yapindula mina zisanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Wachiwiri anabwera ndipo anati, ‘Bwana, ndalama zanu zapindula zisanu zina.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadza waciwiri, nanena, Mbuye, ndalama yanu yapindula ndalama zisanu.