Luke 19:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwo adamuyankha kuti, ‘Pepani, ambuye, ameneyu ali kale ndi ndalama makumi khumi.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa iye, Mbuye, ali nazo mina khumi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati, “Bwana iyeyu ali nazo kale khumi!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa iye, Mbuye, ali nazo ndalama khumi.