Luke 19:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
naŵauza kuti, “Pitani m'mudzi mukuwonawo. Mukakangoloŵamo mukapeza mwanawabulu ali chimangire, amene munthu sanakwerepo chikhalire. Mukammasule, nkubwera naye kuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati, Mukani kumudzi uli pandunji panu; m'menemo, polowa, mudzapeza mwana wa bulu womangidwa, pamenepo palibe munthu anakwerapo nthawi iliyonse; mummasule iye nimumtenge.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pitani mʼmudzi uli patsogolo panu, mukakalowa mʼmudzimo, mukapeza mwana wabulu womangiriridwa amene wina aliyense sanakwerepo. Mukamumasule ndi kubwera naye kuno.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati, Mukani ku mudzi uli pandunji panu; m'menemo, polowa, mudzapeza mwana wa buru womangidwa, pamenepo palibe munthu anakwerapo nthawi iri yonse; mummasule iye nimumtenge.