Luke 19:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wina akakakufunsani kuti, ‘Mukummasuliranji?’ Mukati, ‘Ambuye ali naye ntchito.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthu akati kwa inu, Mummasuliranji? Mudzatero naye, Ambuye amfuna iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati wina aliyense akakufunsani kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani mukumumasula mwana buluyo?’ Mukamuwuze kuti, ‘Ambuye akumufuna.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipomunthuakati kwa inu, Mummasuliranji? mudzatero naye, Ambuye amfuna iye.