Luke 19:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ankamasula mwanawabuluyo, eniake adaŵafunsa kuti, “Mukummasuliranji mwanawabuluyu?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene anamasula mwana wa bulu, eni ake anati kwa iwo, Mumasuliranji mwana wa bulu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ankamasula mwana wabuluyo, eni ake anawafunsa kuti, “Nʼchifukwa chiyani mukumasula mwana wabuluyo?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene anamasula mwana wa buru, eni ace anati kwa iwo, Mumasuliranji mwana wa buru?