Luke 19:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adati, “Ndikutitu iwoŵa akangokhala chete, ifuula ndi miyalayi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayankha nati, Ndinena ndi inu, ngati awa khala chete miyala idzafuula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anayankha kuti, “Ine ndikukuwuzani kuti, ngati atakhala chete, miyala idzafuwula.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayankha nati, Ndinena ndi inu, ngati awa akhala cete miyala idzapfuula.