Luke 19:41 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu atayandikira, nkuwona Yerusalemu, adalira chifukwa cha mzindawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo m'mene anayandikira, anaona mudziwo naulirira,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye atayandikira ku Yerusalemu ndi kuona mzindawo, anawulirira
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo m'meneanayandikira, anaona mudziwo naulirira,