Luke 19:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu adaloŵa m'Nyumba ya Mulungu, nayamba kutulutsa anthu amene ankachita malonda m'menemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analowa m'Kachisi, nayamba kutulutsa iwo akugulitsa malonda, nanena nao,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Iye analowa mʼdera la Nyumba ya Mulungu ndi kuyamba kutulutsa kunja amene amachita malonda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analowa m'Kacisi, nayamba kuturutsa iwo akugulitsa malonda, nanena nao,