Luke 19:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesu ankaphunzitsa m'Nyumba ya Mulungu tsiku ndi tsiku. Akulu a ansembe, aphunzitsi a Malamulo ndiponso akulu a Ayuda ankafuna kumupha,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo analikuphunzitsa m'Kachisi tsiku ndi tsiku. Koma ansembe aakulu, ndi alembi ndi akulu a anthu anafunafuna kumuononga Iye;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lililonse amaphunzitsa mʼNyumba ya Mulungu. Koma akulu a ansembe, aphunzitsi amalamulo ndi atsogoleri pakati pa anthu amayesetsa kuti amuphe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo analikuphunzitsa m'Kacisi tsiku ndi tsiku. Koma ansembe akulu, ndi alembi ndi akulu a anthu anafunafuna kumuononga iye;