Luke 19:48 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
koma adaasoŵa chochita, chifukwa anthu onse ankatengeka nawo mtima mau ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo sanapeze chimene akachita; pakuti anthu onse anamlendewera Iye kuti amve.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe iwo sanathe kupeza njira ina iliyonse kuti achite izi, chifukwa anthu onse anakhulupirira mawu ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo sanapeza cimene akacita; pakuti anthu onse anamlendewera iye kuti amve.